Overview

SPECIAL ANNOUNCEMENT FROM GRANT ZIBA

Dzulo munthu wandibera Laptop HP around Luwinga Township, Mzuzu.

Chonde amene angayioneko or amene amachotsa ma password wina wake akabwera kuti akufuna achosetse password pa laptop plz plz ayimbe pa ma nambala awa:

Grant Ziba: 0999 259 292/ 0999 109 366/ 0881 625 489

Or
David Jere: 0999 211 010/0995 110 057.

A reward will be given.