Overview

Munthu wina dzina lake Dyson Mbendela wataya Driving Liceice. Yatoledwa kumachinjiri kwa Chikapa Blantyre, ngati alipo omwe tikumudziwa Dyson Mbendela mudziwitseni kuti ayimne a number ilimusiyi kuti athe kudzatenga.

Ine ndi Alexander Kundwe ndimakhala Ku Blantyre machinjiri, 0994064200.