JANUARY, 2024 INTAKE AT MALOSSA TECHNICAL COLLEGE MZUZU-CAMPUS
Education & Training
December 2, 2023
Mzuzu, Malawi
December 31, 2023

Company: Malossa Technical College Mzuzu-Campus

Please Share

Overview

MALOSSA TECHNICAL COLLEGE MZUZU-CAMPUS

 

PART A

  • We would like to acknowledge the general public that MALOSSA TECHNICAL COLLEGE MZUZU-CAMPUS will be opening soon, but the classes will start on 03rd January, 2024, course duration is 6 months for Certificate, Diploma and Advanced Diploma. The COURSES on offer are:

 

  1. Electrical and Electronics (City & Guilds)
  2. Refrigeration & Air-Conditioning Mechanics (City & Guilds)
  • For City & Guilds fees is MK200,000.00 practical’s inclusive (Register now for C & G courses at only MK5,000)

           

                                

PART B

  • Malossa Technical College Mzuzu-Campus” ikuperekaso mwai ophunzira ntchito zamanjazi angakhale inu mulibe satifiketi iliyonse kuti mukhale ozidalira panokha. Maphunzirowa ayamba pa 09thDecember, 2023 ndipo mamphunzirowa achitika kwa miyezi itatu, loweruka ndi lamulungu lokhalokha kuti tithe kupereka mwai kwa onse kuti mkati mwasabata atha kupangakonso zina. Maphunzirowa achitikira m’muzinda wa: Mzuzu-Katoto Primary School nthawi yoyambira ndi 8 koloko mamawa mpakana 4:30 madzulo. Mamphunzirowa ndi monga:

 

  1. Kukonza zinthu za Magetsi komanso
  2. Ma Fridge ndi ma Air-conditioners

 

  • Fizi kwa omwe azalandire Certificate ya TEVETA ndi MK100,000.00 (Register now at only 000)
  • Makalasi azayamba anthu akakwana 10
  • Ma Certificate azaperekedwa ndi a TEVETA pokutha pamamphunzirowa

 

MZUZU IS YOUR TIME TO SHINE NOW!!! DON’T MISS THIS OPPORTUNITY

 

For more information you can contact us on 0883-4335-55/098-7700-350/WhatsApp, all City & Guilds courses are full-time, part time as well as weekend are available.