- Type
- Posted on
- Location
- Expiry Date
Company: Excellence Assured
Please Share
Overview
Izi zimasowa , Zisakuphonyeni
Kodi Mumafuna Mutaphunzira Data Entry ndi Data analysis,(SPSS , EXCEL) ndi AKATSWIRI , kuti muimvetse bwino bwino?
Bwerani Pa 24th August, 2024 @ Lilongwe LEA near Simama Hotel (8:00am)
izi zikhoza kutheka , popanda kulipira fees ngati achitira ena koma registration ya K12,500.00 yokha basi, (inuyo musaphwinjike)
*Zokoma zambiri🔥*
Pakatha izi Mudzaphinziranso zina izi *Osalipira Kanthu* (ngakhale registration )
❇️Accounting Softwares (Sage 50 & Quicks Books )
❇️Project Management
❇️Monitoring and Evaluation
❇️Human Resorice Management
Izi akupanga ndi A *Excellence Assured Company*
Contact 0996982449 on Whatsapp!
*Dzuwani!* EXCELLENCE ASSURED imapeleka ma international
Professional certificate omwe akhoza kugwiritsidwa Nchito pofunsira Ntchito kapena kupamga upgrade ..
Tiye tikakomane Komko🔥🔥
*Gawani uthengawu*