SALONIST
Full Time
March 23, 2024
Lilongwe, Malawi
April 5, 2024

Company: Private

Please Share

Overview

POSITION: SALONIST

Ndikufuna mtsikana wamu salon othaka kupanga zose zamu salonย  expert kuma pencil lines, noteless braids...salon ili ku Lilongwe pama Tchansi so akhale from surrounding areas.

NOTE:
โ€ขStarting salary K50,000
โ€ขLunch to be provided.

Oyifuna ntchitoyi ayimbe kapena WhatsApp inbox: 0996 38 18 55.

Tsiku lotseka (Closing date): 5th April 2024.