SECURITY GUARD
Full Time
April 11, 2025
Blantyre, Malawi
April 25, 2025

Company: Private

Please Share

Overview

Tikufuna Mulonda/Security Guard

 

Job Vacancy: Security Guard/ Mulonda, Ku Chigumula. Limbe

Ife timafuna mulonda okhulupirika ndi wa experience ku nyumba kwathu kuchigumula.

Zofunikira

  1. Akhale ndi reference yabwino kwa anthu atatu
  2. Experience yoposa zaka 5
  3. Tikufuna atachokera ku Karonga, Mzuzu, Rumphi, Chitipa kapena Ntcheu

 

Ngati ntchito mwayikonda tumizileni CV kapena message ku manambala awiriwa:

0996115598 ndi 0999917881

 

Mutiwuze kuti:

  1. Mwagwira ntchito kuti ndi kuti
  2. Muli ndi experience ya zaka zingati
  3. Mungayambe liti ntchito
  4. Mungasamuke kuchoka kwanu kudzakhala ku Chigumula

 

Tsiku lotseka advert iyi pa 25th April 2025