Tikufuna wa ntchito ometa/barberman
Full Time
October 19, 2026
Blantyre, Malawi
October 23, 2026

Company: Tafika Barbershop

Please Share

Overview

 

*MWAYI WA NTCHITO*
Tikufuna wa ntchito ometa/barberman

*Zoyenela*
✅Akhale munthu oti anagwira ntchito osachepera zaka ziwiri
✅Osachepera zaka 18 zakubadwa
✅Odziwa bwino kulandila makasitomala
✅Olimbikira pa Ntchito
✅wa Ukhondo
✅Wa kumachinjiri (Jumbe)

*Chidziwitso*
Tikufuna wa kumachinjiri kwa Jumbe, Blantyre.

Ofuna ntchitoyi atumize nambala, dzina ndi zaka pa Whatsapp/local message pa *0997566291* pasanafika pa 23 October 2026

Chonde Osayimba!!!!!